A Ntanyiwa Mubweletse Umboni Pasanathe 72 Hrs - Agape Khombe

Nyasa VoiceBox
Nyasa VoiceBox
36.8 هزار بار بازدید - 4 ماه پیش - On Nyasa VoiceBox, Agape Khombe
On Nyasa VoiceBox, Agape Khombe responds to allegations that he is a drug dealer and is implicated in the death of Ralph Kasambara in Lilongwe. He also warns Comrade Ntanyiwa of Limpopo FM, who made the allegations, about legal action if he does not provide evidence to support his claims. Ku Nyasa VoiceBox, Agape Khombe akutsutsa phekesela yoti ndi wogulitsa mankhwala ndipo akukhudzidwa ndi imfa ya Ralph Kasambara ku Lilongwe. Iye akuchenjezanso Comrade Ntanyiwa wa ku Limpopo FM, yemwe wanena izi, za milandu ngati sapereka umboni wotsimikizira zomwe akunenazo. #malawi
4 ماه پیش در تاریخ 1403/03/25 منتشر شده است.
36,857 بـار بازدید شده
... بیشتر